Gappu Sangathe Kubvina
Aliyense mkalasi la 1A amadziwa kuti Gappu sangathe kubvina. Pamene wophunzira akweza manja ao a manzere, iye akweza dzanja la manja! Kodi aphunzitsi angathe kupangitsa kuti Gappu abvine? Nthano ya chimwemwe chakubvina, kugwiritsa nchito ganizo losiyana.