Mfumukazi yonyamula zitsulo zolemera
Mfumukazi Nila ali ndi chidwi chopambana mu mpikisano wotchuka wonyamula zitsulo zolemera wa Surya, mu ufumu wake. Koma kuli zinthu zambiri zotchinga kuti azipambane. Ndiponso, kusaiwalira kuyembekezera kwa mwana wamwamuna wamfumu wokongola ndi makolo ake.