Easy words, word repetition, less than 250 words
28 books
How does little girl get ready for school?
Who are the different farm animals? Find listed in this book!
A story about reading.
Find out about an unique cow.
Mom is away and Dad is making the morning porridge.
Mungathe kuwerenga kabuku aka, koma simungathe kukazonda! Ndipo ngati ana ang'ono angathe kukawerenga, angathe kukonda zojambula zili mkati mwake.
Uyu ndu Jilly. Lero, wakumabtira achona ambirimbiri mum'zinda.
Amai apita pakamphindi kang'ono. Kodi ndi chiyani chingachitike?
Kodi ndi chiyani ichi? Sichili ngati ine. Kodi uganiza kuti ndi choopsa?
Banja la Thabo liri kukonzekera zochitika mtsiku ndipo zinthu ziri mbwembwembwe pamene alikukonzekera. Nanga Thabo alikuti?
Londi amakonda kulota tsiku lonse. Koma nanga kulota kwake kum'peleka kuti?
Do you know all your body parts? Find out!
By navigating this website, you agree to the storing of cookies on your device to enhance site navigation and analyze site usage.