Your Email*
Your Message
Δ
Pamene anali mtsikana wamng'ono Zanele Situ anauzidwa kuti sadzayendnso. Kukhala mu mphando wa mawilo sikunamletse. Anagwira nchito yaikulu ndi kuphunzira molimbika ndi kupambana za masewero a dziko. Iyi ndi nkhani yake...
Musuku anakolola zambiri kucoka m’munda ndipo anaika zokolola zake munkokwe. Anaika tanje wamkulu pamwamba kuti abise zonse zomwe zinali mnkokwe ndi kulemba cona nchito yokhala malonda. Tanje uyu anali wamkulu womwe sauonepo m’mudzi wa Musuku. Ambiri anakhala ndi cidwi ndi tanje uyu maka-maka nyani omwe anali mbala. Kodi muganiza kuti cona azateteza tanje ndi zokolola zina zonse?
Mnyumba mwa Savana muli zii. Kodi angathe kuchita chiyani kuti mumveke mimvekero? Wayamba kupanga nyimbo zake. Tiyeni timvetsere.
Malita ndi Mailosi ali ndi bokosi lodzala la mandasi. Pamene afuna kudya ...DING"I DONG'U! Oh, mlendo. Ali ndi mandasi khumi ndi awiri. Kodi ndi mandasi angati amene aliyense adzatenga?
Lindi anapeza njobvu yaikulu m'chipinda chake. Nanga ilipodi pamene anthu onse sakhulupilira?
Kanji ali kuphunzira kutchova njika, koma sichapafupi konse! Anali kugwa mopitiriza, mpaka kudzichita. Kodi adaphunzira kutchova njika? Kapena analekera panjira? Nthano yofunditsa mtima pa zofunikira za kuyesa.
By navigating this website, you agree to the storing of cookies on your device to enhance site navigation and analyze site usage.